Ndale zikusokoneza ubale wa m’tsogoleri wa dziko ndi wachiwiri wake – PAC
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Bungwe la Public Affairs Committee (PAC) lati kusagwirizana pakati pa mtsogoleri wa dziko lino ndi wa chiwiri wake, ndichitsimikizo choti m’dziko muno ndale ndizomwe zimagwira ntchito kwambiri kuposa malamulo. Izi ndi malingana ndi woyankhulira bungwe la PAC a Bishop Gilford Matonga omwe anena izi Loweruka pomwe amayankhula ndi imodzi mwa nyumba zowulutsa mawu mdziko muno. […] Read the full artic
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Bungwe la Public Affairs Committee (PAC) lati kusagwirizana pakati pa mtsogoleri wa dziko lino ndi wa chiwiri wake, ndichitsimikizo choti m’dziko muno ndale ndizomwe zimagwira ntchito kwambiri kuposa malamulo. Izi ndi malingana ndi woyankhulira bungwe la PAC a Bishop Gilford Matonga omwe anena izi Loweruka pomwe amayankhula ndi imodzi mwa nyumba zowulutsa mawu mdziko muno. […]
Read the full article and more Malawi news at Ndale zikusokoneza ubale wa m’tsogoleri wa dziko ndi wachiwiri wake – PAC">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 105 words · 1 min read
- Published
- November 15, 2026
- Byline
- William Nsanama
- Source
- Malawi24