Ndinakaba pakhomo pakwawo – Chisale
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Wachiwiri kwa nduna yazachitetezo cha mdziko, Norman Chisale wawuza anthu omwe amanena kuti ndalama zake ndizakuba, kuti nawoso akabe ndie akathandizire anthu ovutika. Chisale wati ndizomvetsa chisoni kuti anthu omwe amalimbirikira kutukwanawa akawagwira amakhala otuwa, akumudzi ndipo zimadabwitsa kuti akuwatuma ndi ndani. Poyankhula ndi Kanema wa Luntha, ndunayi inayankhula izi poyankha fuso lok
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Wachiwiri kwa nduna yazachitetezo cha mdziko, Norman Chisale wawuza anthu omwe amanena kuti ndalama zake ndizakuba, kuti nawoso akabe ndie akathandizire anthu ovutika. Chisale wati ndizomvetsa chisoni kuti anthu omwe amalimbirikira kutukwanawa akawagwira amakhala otuwa, akumudzi ndipo zimadabwitsa kuti akuwatuma ndi ndani. Poyankhula ndi Kanema wa Luntha, ndunayi inayankhula izi poyankha fuso lokhudzana ndi umoyo […]
Read the full article and more Malawi news at Ndinakaba pakhomo pakwawo – Chisale">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 98 words · 1 min read
- Published
- November 15, 2026
- Byline
- Eric Chiputula
- Source
- Malawi24