Munasankha nokha nkhalamba – Namalomba
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Shadric Namalomba wati anthu asiye kulubwalubwa za umoyo wa m’tsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika ponena kuti aMalawi adamusankha okha atamukonda posayang’anira zaka zake chonsecho achinyamata oti nkuwavotera adalipo. Namalomba yemwe ndi nduna ya zofalitsa nkhani komanso woyankhulira boma, wayankhula izi Lachisanu pomwe amayankhula ndi wailesi ya Zodiak. Kuyankhulaku kukudza pomwe anthu ochul
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Shadric Namalomba wati anthu asiye kulubwalubwa za umoyo wa m’tsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika ponena kuti aMalawi adamusankha okha atamukonda posayang’anira zaka zake chonsecho achinyamata oti nkuwavotera adalipo. Namalomba yemwe ndi nduna ya zofalitsa nkhani komanso woyankhulira boma, wayankhula izi Lachisanu pomwe amayankhula ndi wailesi ya Zodiak. Kuyankhulaku kukudza pomwe anthu ochuluka akudzudzula boma […]
Read the full article and more Malawi news at Munasankha nokha nkhalamba – Namalomba">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 98 words · 1 min read
- Published
- November 28, 2026
- Byline
- Lindiwe Sambalikagwa
- Source
- Malawi24