Pepani aMalawi tikukugonekani mu mdima — Namalomba
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Nduna yofalitsa nkhani yemwenso ndi m’neneri wa boma a Shadric Namalomba apepesa mtundu wa aMalawi chifukwa cha kuzimazima kwa magetsi komwe kukuchitika mdziko lino. A Namalomba ati boma likuvomereza kuti likuwagoneka anthu mu mdima. Polankhula ndi wayilesi ya kanema ya Zodiak loweluka a Namalomba ati kuzimazima kwa magetsi ndi vuto lalikulu lomwe akuyesesa kuthana nalo. […] Read the full article
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Nduna yofalitsa nkhani yemwenso ndi m’neneri wa boma a Shadric Namalomba apepesa mtundu wa aMalawi chifukwa cha kuzimazima kwa magetsi komwe kukuchitika mdziko lino. A Namalomba ati boma likuvomereza kuti likuwagoneka anthu mu mdima. Polankhula ndi wayilesi ya kanema ya Zodiak loweluka a Namalomba ati kuzimazima kwa magetsi ndi vuto lalikulu lomwe akuyesesa kuthana nalo. […]
Read the full article and more Malawi news at Pepani aMalawi tikukugonekani mu mdima — Namalomba">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 100 words · 1 min read
- Published
- October 18, 2026
- Byline
- Mphatso Khutcha Richard
- Source
- Malawi24