Mulungu musamumvere Mwanamvekha — Muluzi
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha UDF, Atupele Muluzi wapempha Mulungu kuti asavere zomwe yanena nduna yazachuma a Joseph Mwanamvekha, kuti onyoza utsogoleri wa a Arthur Peter Mutharika adzifa. Muluzi walemba izi pa tsamba lake la Facebook, pomweso wayika kanema wowonetsa a Mwanamvekha akuyankhula ku Mulhako Wa Alhomwe, komwe amadzudzula anthu ena omwe akuti akuchita motsutsana ndi […] Read the
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha UDF, Atupele Muluzi wapempha Mulungu kuti asavere zomwe yanena nduna yazachuma a Joseph Mwanamvekha, kuti onyoza utsogoleri wa a Arthur Peter Mutharika adzifa. Muluzi walemba izi pa tsamba lake la Facebook, pomweso wayika kanema wowonetsa a Mwanamvekha akuyankhula ku Mulhako Wa Alhomwe, komwe amadzudzula anthu ena omwe akuti akuchita motsutsana ndi […]
Read the full article and more Malawi news at Mulungu musamumvere Mwanamvekha — Muluzi">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 98 words · 1 min read
- Published
- October 19, 2026
- Byline
- Eric Chiputula
- Source
- Malawi24