Kwatsala nthawi pang’ono kuti mavutowa athe — Namalomba
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Ngati munataya chikhulupiliro, boma likuti osapanga za nguluwe yolira msampha utaning’a, pomwe lati kwangotsala kanusu chabe kuti mavuto omwe akuta dziko lino athe. Nduna yofalitsa nkhani, Shadric Namalomba wati ndiwokhudzika ndi nyengo zomwe a Malawi akudutsamo monga kusowa kwa mafuta, ndalama zakunja ndi kuvuta kwa magetsi, koma wati anthu asataye mtima pomwe wati mavutowa pompano […] Read the
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Ngati munataya chikhulupiliro, boma likuti osapanga za nguluwe yolira msampha utaning’a, pomwe lati kwangotsala kanusu chabe kuti mavuto omwe akuta dziko lino athe. Nduna yofalitsa nkhani, Shadric Namalomba wati ndiwokhudzika ndi nyengo zomwe a Malawi akudutsamo monga kusowa kwa mafuta, ndalama zakunja ndi kuvuta kwa magetsi, koma wati anthu asataye mtima pomwe wati mavutowa pompano […]
Read the full article and more Malawi news at Kwatsala nthawi pang’ono kuti mavutowa athe — Namalomba">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 101 words · 1 min read
- Published
- October 18, 2026
- Byline
- Eric Chiputula
- Source
- Malawi24