Civil sitimu ya mphamvu kuti timasowa nayo mtendere – Chikhosi
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Mphunzitsi wa timu ya Silver Strikers Ladies, Shadreck Chikhosi wati Civil Women yangochita mwayi kuti yawagonjetsa lero mu NBM Women’s Premiership koma atsikana a m’bomawa sikuti ndi a mphamvu zoti zingawasowetse mtendere kunkhani yolimbirana ukatswiri. Chikhosi amayankhula izi atangotha masewero omwe timu yake yafa ndizigoli zitatu kwa ziwiri mmanja mwa Civil pa bwalo la Silver […] Read the ful
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Mphunzitsi wa timu ya Silver Strikers Ladies, Shadreck Chikhosi wati Civil Women yangochita mwayi kuti yawagonjetsa lero mu NBM Women’s Premiership koma atsikana a m’bomawa sikuti ndi a mphamvu zoti zingawasowetse mtendere kunkhani yolimbirana ukatswiri. Chikhosi amayankhula izi atangotha masewero omwe timu yake yafa ndizigoli zitatu kwa ziwiri mmanja mwa Civil pa bwalo la Silver […]
Read the full article and more Malawi news at Civil sitimu ya mphamvu kuti timasowa nayo mtendere – Chikhosi">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 103 words · 1 min read
- Published
- October 18, 2026
- Byline
- Eric Chiputula
- Source
- Malawi24