Munthu ukakula umayenera uvomereze — Muluzi
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Mtsogoleri wa chipani cha UDF, Atupele Muluzi wati amalemekeza kwambiri m’tsogoleri wa dziko lino, Peter Mutharika koma wati ndikofunika kuvomereza kukula kwawo. Muluzi wanena izi pamene amacheza pa wayilesi ya kanema ya Zodiak, nkati mwa pulogalamu ina. “Ine ndine m’modzi amene ndinagwira ntchito ndi President Professor Arthur Peter Mutharika, ndagwira nawo ntchito dzaka ngati Nduna, […] Read th
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Mtsogoleri wa chipani cha UDF, Atupele Muluzi wati amalemekeza kwambiri m’tsogoleri wa dziko lino, Peter Mutharika koma wati ndikofunika kuvomereza kukula kwawo. Muluzi wanena izi pamene amacheza pa wayilesi ya kanema ya Zodiak, nkati mwa pulogalamu ina. “Ine ndine m’modzi amene ndinagwira ntchito ndi President Professor Arthur Peter Mutharika, ndagwira nawo ntchito dzaka ngati Nduna, […]
Read the full article and more Malawi news at Munthu ukakula umayenera uvomereze — Muluzi">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 99 words · 1 min read
- Published
- September 30, 2026
- Byline
- William Nsanama
- Source
- Malawi24