Adindo achenjezedwa pa zitukuko za kaphulira za CDF
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Adindo m’boma la Kasungu awapempha kuti awonetsetse kuti zitukuko zonse za pansi pa thumba lakudera, Reformed Constituency Development Fund (RCDF) zisachitike mwakaphulira, ponena kuti ndalama za a Malawi zikuyenera kugwira ntchito bwino. Phungu wadera la Kasungu Manisipalite, Noel Mkubwi wati zidzakhala zoipa kuti pomwe boma likupereka ndalama za chitukuko zochuluka kulipira ma kontilakitala ken
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Adindo m’boma la Kasungu awapempha kuti awonetsetse kuti zitukuko zonse za pansi pa thumba lakudera, Reformed Constituency Development Fund (RCDF) zisachitike mwakaphulira, ponena kuti ndalama za a Malawi zikuyenera kugwira ntchito bwino. Phungu wadera la Kasungu Manisipalite, Noel Mkubwi wati zidzakhala zoipa kuti pomwe boma likupereka ndalama za chitukuko zochuluka kulipira ma kontilakitala kenako chitukukocho […]
Read the full article and more Malawi news at Adindo achenjezedwa pa zitukuko za kaphulira za CDF">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 101 words · 1 min read
- Published
- October 21, 2026
- Byline
- Ben Bongololo
- Source
- Malawi24