Joe Ikon avulala atadziponya pa siteji
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Mawu woti timba anathyoka mwendo dansi yothaitha aphelezela pa woyimba Joe Ikon yemwe wavulala atichita ukandiyerekere pagulu podziponya pa nsanja. Woyimbayu anali ndi phwando la mayimbidwe Loweruka munzinda wa Blantyre lomwe amalitcha kuti “Mwana wa Atate” komwe khwimbi linasonkhana. Kamena wina yemwe akuzungulila pa masamba amchezo, akuonesa Ikon akuchoka pa nsanja ndikudziponya ku malo omwe […
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Mawu woti timba anathyoka mwendo dansi yothaitha aphelezela pa woyimba Joe Ikon yemwe wavulala atichita ukandiyerekere pagulu podziponya pa nsanja. Woyimbayu anali ndi phwando la mayimbidwe Loweruka munzinda wa Blantyre lomwe amalitcha kuti “Mwana wa Atate” komwe khwimbi linasonkhana. Kamena wina yemwe akuzungulila pa masamba amchezo, akuonesa Ikon akuchoka pa nsanja ndikudziponya ku malo omwe […]
Read the full article and more Malawi news at Joe Ikon avulala atadziponya pa siteji">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 99 words · 1 min read
- Published
- October 25, 2026
- Byline
- Joseph Mphiya
- Source
- Malawi24