Bob wauzidwa kuti Noma itenge ligi
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Nyerere pakatipa zayenda mwa pendapenda pang’ono, koma zimenezo mtsogoleri wake Thom Mpinganjira sizikumukhudza ngakhale pang’ono. Iye wauza mphunzitsi wa Mighty Wanderers Bob Mpinganjira kuti ngakhale kubwere mvula kapena kuombe dzuwa, FDH Premiership ilowere ku Lali Luban. Thom wati khumbo lake ndiloti pomwe chaka chamawa chino Wanderers ikhale ikusangalala kuti yakwanitsa zaka 65 chikhazikitsi
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Nyerere pakatipa zayenda mwa pendapenda pang’ono, koma zimenezo mtsogoleri wake Thom Mpinganjira sizikumukhudza ngakhale pang’ono. Iye wauza mphunzitsi wa Mighty Wanderers Bob Mpinganjira kuti ngakhale kubwere mvula kapena kuombe dzuwa, FDH Premiership ilowere ku Lali Luban. Thom wati khumbo lake ndiloti pomwe chaka chamawa chino Wanderers ikhale ikusangalala kuti yakwanitsa zaka 65 chikhazikitsidwireni, idzakhale ndi […]
Read the full article and more Malawi news at Bob wauzidwa kuti Noma itenge ligi">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 99 words · 1 min read
- Published
- November 4, 2026
- Byline
- Mphatso Khutcha Richard
- Source
- Malawi24