Zomwe zinachitikapo kale sizingapose malamulo a dziko: MLS ikukhonza
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Bungwe la Malawi Law Society (MLS) liyenera kusapotedwa chifukwa chotsutsa ganizo la Pulezidenti Peter Mutharika loyimitsa yekha msonkhano wa Nyumba ya Malamulo wokambirana za momwe bajeti ya chaka cha 2026 ikuyendera pakati pa chaka. Maganizo a bungweli sakukhudzana ndi kukondera zipani za ndale. Cholinga chake ndi kuteteza malamulo oyendetsera dziko komanso kuonetsetsa kuti palibe Pulezidenti [
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Bungwe la Malawi Law Society (MLS) liyenera kusapotedwa chifukwa chotsutsa ganizo la Pulezidenti Peter Mutharika loyimitsa yekha msonkhano wa Nyumba ya Malamulo wokambirana za momwe bajeti ya chaka cha 2026 ikuyendera pakati pa chaka. Maganizo a bungweli sakukhudzana ndi kukondera zipani za ndale. Cholinga chake ndi kuteteza malamulo oyendetsera dziko komanso kuonetsetsa kuti palibe Pulezidenti […]
Read the full article and more Malawi news at Zomwe zinachitikapo kale sizingapose malamulo a dziko: MLS ikukhonza">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 102 words · 1 min read
- Published
- November 3, 2026
- Byline
- Archangel Nzangaya
- Source
- Malawi24