A Namalomba akufuna umboni ngati ndani? – Suleman
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Kwakhwithima! Ndipo mawere awirirana! Kusagwirizana kwa akuluakulu aboma kwafika mlingo wina tsopano pomwe sipikala wa nyumba yamalamulo, Sameer Suleman wabweza moto kwa a Shadric Namalomba. “Kodi a Namalomba akufuna umboni ngati ndani? A Namalomba asanduka liti wapolisi kapena wa ACB? Awa ndi ena mwa mafunso omwe achoka kwa sipikala kupita kwa nduna yofalitsa nkhaniyi. Chatsitsa […] Read the ful
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Kwakhwithima! Ndipo mawere awirirana! Kusagwirizana kwa akuluakulu aboma kwafika mlingo wina tsopano pomwe sipikala wa nyumba yamalamulo, Sameer Suleman wabweza moto kwa a Shadric Namalomba. “Kodi a Namalomba akufuna umboni ngati ndani? A Namalomba asanduka liti wapolisi kapena wa ACB? Awa ndi ena mwa mafunso omwe achoka kwa sipikala kupita kwa nduna yofalitsa nkhaniyi. Chatsitsa […]
Read the full article and more Malawi news at A Namalomba akufuna umboni ngati ndani? – Suleman">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 101 words · 1 min read
- Published
- October 20, 2026
- Byline
- Eric Chiputula
- Source
- Malawi24