Ena akuikira kumbuyo bambo wokumba manda ake
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Pomwe kwa ena ndi mwikho, ambiri maka pa masamba amchezo ati sakuwonapo vuto ndi zomwe ikuchita njonda ina ku Dowa yomwe ikukumbiratu dzenje lomwe anthu ambiri safuna ataliwona. Faidoni Benamu Kalitsiro wazaka 78, wadodometsa anthu pomwe wayamba ntchito yokumba manda ake m’mudzi wa Makwani m’dera la mfumu yayikulu Dzoole m’bomali. Benamu Kalitsiro wati ntchito yokumba […] Read the full article an
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Pomwe kwa ena ndi mwikho, ambiri maka pa masamba amchezo ati sakuwonapo vuto ndi zomwe ikuchita njonda ina ku Dowa yomwe ikukumbiratu dzenje lomwe anthu ambiri safuna ataliwona. Faidoni Benamu Kalitsiro wazaka 78, wadodometsa anthu pomwe wayamba ntchito yokumba manda ake m’mudzi wa Makwani m’dera la mfumu yayikulu Dzoole m’bomali. Benamu Kalitsiro wati ntchito yokumba […]
Read the full article and more Malawi news at Ena akuikira kumbuyo bambo wokumba manda ake">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 100 words · 1 min read
- Published
- September 15, 2026
- Byline
- Ben Bongololo
- Source
- Malawi24