Mneneri ankandiyamwitsa njoka — Waulura msungwana wina
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Pomwe mukupita kumapemphero lero, Kodi mwamva? Zaka pafupifupi khumi zapitazo, msungwana wina wotchuka ndi zisudzo pa TikTok, anagwa mchikondi ndi mneneri wa ‘mulungu’, koma mhuu! Mathero ake n’ngachabe. Pomwe iye amanyadira kuti anali mayi pulofeti, sadadziwe kuti kukada amakhala ‘mayi chinjoka.’ Kupatula kugonana ndi munthu wa ‘mulungu’yo, mabere ake ankagwiritsidwaso ntchito zina. Walinase Chi
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Pomwe mukupita kumapemphero lero, Kodi mwamva? Zaka pafupifupi khumi zapitazo, msungwana wina wotchuka ndi zisudzo pa TikTok, anagwa mchikondi ndi mneneri wa ‘mulungu’, koma mhuu! Mathero ake n’ngachabe. Pomwe iye amanyadira kuti anali mayi pulofeti, sadadziwe kuti kukada amakhala ‘mayi chinjoka.’ Kupatula kugonana ndi munthu wa ‘mulungu’yo, mabere ake ankagwiritsidwaso ntchito zina. Walinase Chisanu, yemwe […]
Read the full article and more Malawi news at Mneneri ankandiyamwitsa njoka — Waulura msungwana wina">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 100 words · 1 min read
- Published
- September 27, 2026
- Byline
- Eric Chiputula
- Source
- Malawi24