BEAM yapulumutsa wophunzira ku UNIMA
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Patangodutsa masiku ochepa Malawi24 italemba nkhani ya Joseph Nenani Major, wophunzira wa ku University ya Malawi UNIMA yemwe amafuna kudzipha kaamba ka mavuto ndi ngongole, Mayi wa fuko, Gertrude Mutharika wadalitsa wophunzirayu. Mkazi wa mtsogoleri wa dzikoyu wati anakhudzika kwambiri atamva moyo omwe ophunzirayu amakhala kuyambira pomwe anayamba maphunziro ake mchaka choyamba. Kutsatira izi, k
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Patangodutsa masiku ochepa Malawi24 italemba nkhani ya Joseph Nenani Major, wophunzira wa ku University ya Malawi UNIMA yemwe amafuna kudzipha kaamba ka mavuto ndi ngongole, Mayi wa fuko, Gertrude Mutharika wadalitsa wophunzirayu. Mkazi wa mtsogoleri wa dzikoyu wati anakhudzika kwambiri atamva moyo omwe ophunzirayu amakhala kuyambira pomwe anayamba maphunziro ake mchaka choyamba. Kutsatira izi, kudzera […]
Read the full article and more Malawi news at BEAM yapulumutsa wophunzira ku UNIMA">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 98 words · 1 min read
- Published
- October 15, 2026
- Byline
- Mphatso Khutcha Richard
- Source
- Malawi24