Makoponi afika ku Kasungu
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Kuli chimwemwe kwa alimi pafupifupi 50,000 m’boma la Kasungu pomwe makoponi pansi pa ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya Farm Inputs Subsidy Program (FISP), afika tsopano. Boma la Kasungu lalandira makoponi omwe alimi okwana 48,596 omwe adalembetsedwa agwiritse ntchito pogulira feteleza mu ndondomeko ya FISP. A Loveness Kapachika omwe anayimira bwanamkubwa wabomali a […] Read the f
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Kuli chimwemwe kwa alimi pafupifupi 50,000 m’boma la Kasungu pomwe makoponi pansi pa ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya Farm Inputs Subsidy Program (FISP), afika tsopano. Boma la Kasungu lalandira makoponi omwe alimi okwana 48,596 omwe adalembetsedwa agwiritse ntchito pogulira feteleza mu ndondomeko ya FISP. A Loveness Kapachika omwe anayimira bwanamkubwa wabomali a […]
Read the full article and more Malawi news at Makoponi afika ku Kasungu">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 97 words · 1 min read
- Published
- October 4, 2026
- Byline
- Ben Bongololo
- Source
- Malawi24