Tikufuna tisiye kuchinyitsa kwambiri – Ekhaya
This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Pomwe ligi yaikulu ya FDH Premiership ikubwerera m’bwalo lero, matimu achenjezedwa ofuna pagolo pa Ekhaya avale dzilimbe apo bii sapaona. Mphunzitsi wa Ekhaya Fundi Akidu, wati limodzi mwa vuto lomwe timuyi yakumana nalo mchigawo choyamba chapitachi, ndilogoletsetsa zigoli zochuluka. Akidu amalunkhula izi Lachisanu pomwe Ekhaya ikuyembekezeka kuzepulana ndi Kamuzu Barracks lero Loweluka pa bwalo
AI summary
This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Pomwe ligi yaikulu ya FDH Premiership ikubwerera m’bwalo lero, matimu achenjezedwa ofuna pagolo pa Ekhaya avale dzilimbe apo bii sapaona. Mphunzitsi wa Ekhaya Fundi Akidu, wati limodzi mwa vuto lomwe timuyi yakumana nalo mchigawo choyamba chapitachi, ndilogoletsetsa zigoli zochuluka. Akidu amalunkhula izi Lachisanu pomwe Ekhaya ikuyembekezeka kuzepulana ndi Kamuzu Barracks lero Loweluka pa bwalo la […]
Read the full article and more Malawi news at Tikufuna tisiye kuchinyitsa kwambiri – Ekhaya">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Follow the story
About this article
- Length
- 99 words · 1 min read
- Published
- October 10, 2026
- Byline
- Mphatso Khutcha Richard
- Source
- Malawi24